Chichewa and Other Languages
FMA Ntchisi Chanika Block- Chichewa
Ndondomeko yopereka mphavu ndi udindo kwa anthu zosamalira nkhalango zotetezedwa, ndi kugwiritsa bwino ntchito zinthu zopezeka mnenemo
FMA Ntchisi Chifwerekete Block- Chichewa
Ndondomeko yopereka mphavu ndi udindo kwa anthu zosamalira nkhalango zotetezedwa, ndi kugwiritsa bwino ntchito zinthu zopezeka mnenemo
FMA Ntchisi Chifwerekete I and II Block- Chichewa
Ndondomeko yopereka mphavu ndi udindo kwa anthu zosamalira nkhalango zotetezedwa, ndi kugwiritsa bwino ntchito zinthu zopezeka mnenemo
FMA Ntchisi Mpamira Block- Chichewa
Ndondomeko yopereka mphavu ndi udindo kwa anthu zosamalira nkhalango zotetezedwa, ndi kugwiritsa bwino ntchito zinthu zopezeka mnenemo
FMA Ntchisi Mponda Block- Chichewa
Ndondomeko yopereka mphavu ndi udindo kwa anthu zosamalira nkhalango zotetezedwa, ndi kugwiritsa bwino ntchito zinthu zopezeka mnenemo
FMA Ntchisi Msankhire Block- Chichewa
Ndondomeko yopereka mphavu ndi udindo kwa anthu zosamalira nkhalango zotetezedwa, ndi kugwiritsa bwino ntchito zinthu zopezeka mnenemo
FMA Ntchisi Nyanga Block- Chichewa
A management plan to facilitate community management of forests and access to forest resources on public and customary land
FMA Ntchisi Nyanja Block- Chichewa
Ndondomeko yopereka mphavu ndi udindo kwa anthu zosamalira nkhalango zotetezedwa, ndi kugwiritsa bwino ntchito zinthu zopezeka mnenemo
Kugwiriska ntchito nthowa za kalyero zakwenera kuti tilizge panthazi thadzi la bamama na bana
Buku ili lina na uthenga gha ndondomeko izo zikulutisya pa nthazi vyakukhumbikwa pa karyelo kakwenela.
Ndondomeko yikuru mwakudumura yakudangilira ntchito yakulimbikiska kulya kwakwenelera nakwakukwanira
Kabuku ka ndondomeko zapadera zomwe ziwongolere ntchito yolimbikitsa kadyedwe koyenera mdziko muno
Bukhu Lothandizira Kulondoloza Ntchito za Migodi
Bukhu lofotokoza ndondomeko zoyenera kutsatidwa ndi olondoloza komanso ogwira ntchito za migodi. A mining accountability monitoring tool.
A Summary of the Malawi National Guidelines on Integrated Catchment Management and Rural Infrastructure
A combined Chichewa and English summary of the national guidelines on integrated catchment management in Malawi.These guidelines address the environmental issues identified in Malawi's National Environmental Action Plan (NEAP) which are: soil erosion, deforestation, water resources degradation and depletion, threat to fish resources, threat to biodiversity, human habitat degradation, high population growth, air pollution and climate change.
Tiyeni Titenge Mbali Poteteza Nkhalango Zathu
Bukuli likufotokoza zakufunika kwa nkhalango mu dziko lathu. Komanso kupereka maganizo panjira zimene anthu tingatengepo mbali kuteteza nkhalango zathu.
Kuphika Mwamakono Kuti Nkhalango Zathu Zitetezeke
Bukuli likufotokoza za ubale wa nkhalango ndi mphavu zamagesi ophikira ndi kutenthesera pakhomo. Likupereka maganizo panjira zimene anthu tingatengepo mbali kuteteza nkhalango zathu pakugwirisa ntchito njira zamakono zophikira ndikutenthesera.